MABUGWE OMWE SIABOMA KU MCHINJI ATI NDIKOFUNIKA KUTI ANTHU ADZITENGA NAWO GAWO
Mabugwe omwe siaboma m`boma la mchinji ati ndikofunika kuti anthu adzitenga nawo gawo pakuyendetsedwe kazitukuko zomwe zikuchitika m`bomali Malingana ndi wachiwiri Wamkulu…